2025 APM MY VOTE

2025 APM MY VOTE

Share

The right to change the life of Malawians

22/09/2024

Zonse chifukwa chosawa ulamuliro wabwino😭💔

Oyendetsa galimoto ena komanso achibale a dalaiva yemwe zikumveka kuti waombeledwa ndi apolisi pa road block ya 4 miles ku Zomba ayamba kusonkhana ku polisi ya Zomba.

Titafika pamalopa tapeza achibale a malemuwa akulira pa polisiyi ndipo oyendetsa galimoto ataima pa polisiyi.

Ena mwa omwe anali nawo mgalimotoyi padakali pano akuwalemba ma statement.

Wolemba Tiyese Monjeza.

Copied (times 360 Malawi)

21/09/2024

Arthur Peter Mutharika vote yathu

21/09/2024

Inu tikutitu 2025 APM MY VOTE with Madam first lady kuvala zoziwa🔥✨

Don't forget to follow for more information

21/09/2024

Zosatira za mitsonkhano ya DPP ndi MCP zayamba kufika kuno

Omwe akuonera ntsonkhano wa DPP pa times ndi 4.1K

Pomwe akuonera wa MCP pa times ndi 947

Kkkkkkkk boma layamba kuoneka lokha

21/09/2024

Happening now in North

Don't forget to follow 2025 APM MY VOTE for more information...🔥🔥 Akumva pain wina

21/09/2024
21/09/2024

Welcome to 2025 2025 APM MY VOTE ✅

Want your business to be the top-listed Government Service in Blantyre?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Category

Address

Post Office Box 256 Blantyre
Blantyre
556688