Department of Disaster Management Affairs

Call Website Contact the organization

Department of Disaster Management Affairs A Malawi Government agency for coordinating and directing the implementation of DRM programmes

Today we celebrate Mothers Happy Mother’s Day 🥳
15/10/2026

Today we celebrate Mothers
Happy Mother’s Day 🥳

12/10/2026

Dzulo, Pa 11 October, 2026, sitima ya MV Chambo inachita ngozi pakati pa 04:00 ndi 05:00 mamawa, pafupi ndi doko la Mbamba Bay, pa Nyanja ya Malawi. Zatsikimizika kuti pa ngoziyi anthu atatu atisiya.

Sitimayi yomwe ndi ya ku Mozambique, inali paulendo kuchokera ku Mbamba Bay ku Tanzania kupita ku Ntengula ku Mozambique pamene inayaka moto ndipo kenako inamira. Malipoti akusonyeza kuti mu sitimayi munali anthu pafupifupi 42, ndipo mwa anthu amenewa, asanu ndi awiri anali ogwira ntchito m’sitimayo.

Anthu omwe atisiya pa ngoziyi ndi mayi m’modzi wachikulire wa ku Malawi wochokera m’boma la Likoma, mwana wa miyezi itatu wa ku Mozambique, komanso munthu wam’muna yemwe padakali pano sakudziwika. Anthu omwe anapulumuka pangoziyi analandira thandizo la chipatala ku Tanzania.

Ma lipoti oyamba akusonyeza kuti mawaya amagetsi omwe anali osatetezedwa bwino ndi amene anayambitsa motowo. Powonjezera apo, mphepo yamphamvu yomwe inali panyanjayi komanso katundu amene sitimayo inanyamula, kuphatikizapo migolo ya mafuta a petulo ndi dizilo, zinathandizanso kuti motowo ufalikire. Pakadali pano chifukwa chenicheni chomwe chachititsa ngoziyi chikufufuzidwabe.

Boma la Malawi likupepesa mabanja onse amene ataya achibale awo pa ngoziyi. Boma likuthokozanso anthu onse amene anathandiza anthu omwe akhudzidwa ndi ngoziyi.

Malawi News Agency
MBC Digital
Zodiak Online
Times 360 Malawi
Malawi Government
MIJ Online
Nation Publications Limited
TWR Malawi
Luntha television
Mibawa TV
Malawi Red Cross Society - MRCS
Capital FM Malawi
Nkhoma Synod Radio
Radio Maria Malawi
Ministry of Local Government and Rural Development-Malawi

This week, the Department of Disaster Management Affairs (DoDMA) received 9,872 bags of rice from the Government of the ...
09/10/2026

This week, the Department of Disaster Management Affairs (DoDMA) received 9,872 bags of rice from the Government of the People's Republic of China.

This shipment is part of China's US3 million emergency food aid commitment announced in July, marking another vital step in reaching vulnerable communities across Malawi. It follows an earlier contribution of over US4 million in food assistance announced in January.

We express our sincere gratitude to the Chinese Government for its steadfast solidarity and continuous support in times of need.

Malawi News Agency
MBC Digital
Times 360 Malawi
Zodiak Online
MIJ Online
TWR Malawi
Ministry of Local Government and Rural Development-Malawi
Nkhoma Synod Radio
Malawi Government
Luntha television
Capital FM Malawi

01/10/2026

The Government of Malawi has developed the 2026/2027 National El Niño Preparedness Plan to safeguard lives, livelihoods, and socio‑economic development against the anticipated impacts of El Niño.

This Plan provides a coordinated framework for preparedness, anticipatory action, response planning, and resource mobilization across key sectors including agriculture, food security, health, education, water and sanitation, energy, and disaster response.

Get the full plan here: https://dih.immalawi.org/home

Together, let us strengthen national resilience and ensure Malawi is ready to face the challenges ahead.

Malawi News Agency
MBC Digital
Times 360 Malawi
Zodiak Online
Nation Publications Limited
MIJ Online
TWR Malawi
Luntha television
Mibawa TV
Capital FM Malawi
Nkhoma Synod Radio
Malawi Government
Ministry of Local Government and Rural Development-Malawi

The Department of Disaster Management Affairs (DoDMA) has received a vehicle from the European Civil Protection and Huma...
29/09/2026

The Department of Disaster Management Affairs (DoDMA) has received a vehicle from the European Civil Protection and Humanitarian Aid Operations (ECHO), in partnership with the European Union (EU) and the United Nations Development Programme (UNDP).

The vehicle was provided through a 2.5-year project aimed at improving disaster preparedness in Mzuzu, Blantyre, Lilongwe and Zomba. It will help DoDMA respond quickly and reach affected areas when early weather warnings are issued.

UNDP Resident Representative Fenella Frost said the project had already delivered impact-based flood forecasting and improved drainage systems, benefiting more than 198,000 people.
“Although the vehicle is the tangible asset we are handing over today, it represents something much bigger. It is an investment in DoDMA’s ability to prepare for, anticipate and respond to disasters,” she said.

EU Ambassador Daniel Aristi Gaztelumendi said reliable transport and the capacity to act quickly were important when responding to climate-related emergencies and El Niño.
“This ceremony may focus on one vehicle, but it speaks to something much bigger. It speaks to preparedness. And preparedness saves lives,” he said.

DoDMA Commissioner Wilson Moleni said the government was committed to maintaining the vehicle and other disaster-response assets, drawing lessons from Tropical Cyclone Freddy.
“This vehicle is more than just transport. It will support disaster preparedness, early warnings, early action, assessments, coordination and emergency response,” he said.

MBC Digital
Times 360 Malawi
Zodiak Online
Luntha television
Capital FM Malawi
Nation Publications Limited
Mibawa TV
Malawi News Agency
TWR Malawi
MIJ Online
Ministry of Local Government and Rural Development-Malawi
Malawi Government

19/09/2026

Downscaled Seasonal Climate Outlook

18/09/2026

Dzana pa (16/9/2026), Mlembi wa Mkulu wa Boma Dr. Justin Saidi anatsogolera mwambo wopereka ndalama kwa amayi omwe adathawa zipolowe zomwe zimachitikira anthu amayiko ena m'dziko la South Africa.
Kanemayu akuwonetsa tsatanetsatane wa mwambowu.

Malawi News Agency
MBC Digital
Times 360 Malawi
Zodiak Online
Malawi Government
Nation Publications Limited
MIJ Online
Luntha television
Mibawa TV
Malawi Red Cross Society - MRCS
Ministry of Local Government and Rural Development-Malawi

Kunali Chimwemwe chodzadza tsaya kwa mfumu yayikulu Chimwala m'boma la Mangochi pomwe boma mogwirizana ndi bungwe la Ash...
16/09/2026

Kunali Chimwemwe chodzadza tsaya kwa mfumu yayikulu Chimwala m'boma la Mangochi pomwe boma mogwirizana ndi bungwe la Ashraful Aid limapereka thandizo la ndalama kwa amayi omwe adathawa zipolowe zomwe zimachitikira anthu amayiko ena mdziko la South Africa.

Mlembi wankulu wa boma Dr. Justin Said ndi omwe akhazikitsa ntchitoyi lero yomwe ifikire amayi oposera 500 m'bomali.

"Ngati boma tikuthokoza Ashraful Aid chifukwa cha thandizoli. Ndipo ena atengerepo chitsanzo kuti tonse pamodzi titeteze nzika zathu," anatero a Dr. Saidi.

M'modzi mwa akuluakulu ku bungwe la Ashraful Aid, a Ishmael Ngongondo ati bungwe lawo ndilodzipereka kuthandizana ndi boma pa ntchito yoonetsetsa kuti a Malawi omwe adabwera kuchokera ku South Africa azipezere zochita.

M'modzi mwa amayi omwe apindula nawo ndi thandizoli a Mary Kasenda, athokoza boma chifukwa chowathandiza kuti achoke mdziko la South Africa ndi kubwera kuno kumudzi. Iwo ati ndalama yomwe alandira iwathandiza kuyamba business yomwe ankachita asanapite ku South Africa.

Ashraful Aid igwiritsa ndalama zokwana 50 million Kwacha pa ntchitoyi ndipo mayi aliyense alandira 90 sauzande ngati Mpamba.

MBC Digital
Times 360 Malawi
Zodiak Online
Malawi News Agency
MIJ Online
TWR Malawi
Nation Publications Limited
Radio Maria Malawi
Capital FM Malawi
Luntha television

Address

Department Of Disaster Management Affairs, P/Bag 336, Lilongwe 3
Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Department of Disaster Management Affairs posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Organization

Send a message to Department of Disaster Management Affairs:

Shortcuts

Share