Congress Church
Mbewe wa Dzalanyama ndi liwu la Isaiah Emmanuel Sunganimoyo yemwe amayankhula pa nkhani za ndale, zipembedzo, uzimu, chikhalidwe ndi mbiri ya anthu.
06/06/2026
Next President of the Malawi Congress Party (MCP) after Dr. Lazarus McCarthy Chakwera in 2040. Wina atsutse tione!
06/06/2026
Mchewa ndi Mchewa basi, sangasinthe mawanga ake. Mbewe wa Dzalanyama ndi Nyama Zake mu 2020.
Pa 7 June 2026 ndidzayankhulapo pa nkhani yomwe McFarlane Mgwirinji wayankhula, izi ndiyankhula kutsatira pa zomwe iyeyo adanena tili ku Maula Prison. Mudzakhale pomwepo.
Program yotsatira ndi ya nyimbo za ku khosi kwanu. Kwina tikhala tikucheza za nkhani za ku ndende. Kodi moyo wa ku ndende ndi wotani? Kodi amagonana amuna okha okha monga timamvera? From 1pm to pm. 0999806870
Kodi moyo wa ku ndende ndi wotani? Kodi amagonana amuna okha okha monga timamvera?
Program ya lero Tikamba Zomwe yayankhula mfumu Ina ya ku Nsanje. Zikuonetsa kuti Amalawi cheni cheni chomwe timafuna sitimachidziwa.
Sankhani nyimbo ya ku mtima kwanu tumizani smsku 0999806870 kapena mu comment section, tikhala live pano mpaka 2:15pm. NENANI DZINA LANU, DERA LOMWE MULI. NANGA BOMA MUKULIONA BWANJI?
Lero tikamba za ku Prison. Maka ndiyankha funso lakuti kumeneko amuna amagonana? Eya ndi zoonadi koma kodi zimakhala motani? Ndipo amagonedwa ndi ndani?
Click here to claim your Sponsored Listing.
Location
Website
Address
Lilongwe
265
