Yellow Press

Yellow Press

Share

Latest News and Information from Mighty United Democratic Front - UDF

30/04/2026

Same Whatsapp group

22/04/2026

21/04/2026

Mpatseni chinthuchi akonze Atupele Muluzi

Photos from Yellow Press 's post 21/04/2026

Akatundu awawa amaganiza mokuya kwambiri. Akuchita kupelekera ma solutions, sizomangokamba chifukwa ali ku opposition, no, koma kupeleka ma solutions ku boma kuti Amalawi akhale pa bwimo. Chifukwa osanamizana malawi akufunikira Atupele Muluzi basi kuti zinthu ziyende.

21/04/2026

We are facing what is likely the largest oversupply of to***co in our region’s history. Market forces alone could push prices to record lows, placing immense pressure on our farmers.

This situation demands urgent and practical solutions on how we support those who depend on to***co for their livelihoods.

The challenge is made worse by our exchange rate distortions. Farmers are being paid at the official rate, often discounted by up to 30%, while the cost of many goods is already aligned to parallel market rates. This imbalance is deeply unfair and economically damaging.

There is an urgent need to realign our exchange rate framework. The current situation is simply unsustainable. We need urgent reforms.

Rt Hon Atupele muluzi on to***co prices

Photos from Yellow Press 's post 20/04/2026

Mtsogoleri wa Chipani cha UDF, Rt. Hon. Atupele Muluzi, dzulo pa 19 April anali nawo pa Maliro a Senior Chief Inkosi Champiti kwa Champiti Headquarters ku Ntcheu.

A Muluzi ati, Mfumuyi inali yolimba mtima komanso yachilungamo panufumu wawo omwe omwe wakhala kwa zaka 41.

Olemekezeka a Atupele Muluzi anali pamodzi ndi nduna za boma a Norman Chisale komanso a Ben Phiri mwa ena.

19/04/2026

Statement from our SG πŸ’›

Photos from Yellow Press 's post 08/04/2026

Kukunga ticket ya 2030. πŸ’›πŸ’›πŸ’›πŸ₯³πŸ₯³πŸ₯³

03/04/2026

πŸ’›πŸ’›πŸ°πŸ°πŸ£πŸ£ Happy Easter Holidays

01/04/2026

Ku Mpoto πŸ’›

Pakati πŸ’›

Nanga ku M'mwera? πŸ’›

πŸ’›πŸ’›πŸ’› Boma!!!!!

LyolyolyoπŸ’›πŸ’›πŸ₯³πŸ₯³

31/03/2026

Jersey yafika kwa amene anali mwini wake wa Team ya Big Bullets nthawi imeneyo ili Bakili BulletsπŸ‘‘πŸ‘‘πŸ₯³πŸ₯³

Want your business to be the top-listed Government Service in Lilongwe?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Address

Kaunda Road
Lilongwe
0000