06/06/2026
Ili ndi tsiku lomwe anthu a kwa zuze anadala ndi Nduna ya dziko la Ireland komaso kazembe wadziko la Ireland mudzi mwa Gvh Zuze. Iwo anazayendera ntchito za ulimi wa mthilila wa kachewere motsogozedwa ndi Bungwe la Self Help.
06/06/2026
Youths are leaders of today.
Mwaswera bwanji uko muli?
Mbali za kuchimbiya Dedza Linthipe Constituency.. kuno mvula yokha koma taswera bwino
25/05/2026
Dedza Linthipe Constituency.. zingayambe kuyiwalika
Kucheza ndi magogo pa nkhani za chitukuko.
Mwadzuka bwanj ?
25/05/2026
Trust process, one day things will never be the same again
Dedza Linthipe Constituency..