EFF Malawi Secretary General Paul Kanyimbo

EFF Malawi Secretary General Paul Kanyimbo

Share

General Dealer

22/11/2025

Tamangotipatsani ngongolezo ma business certificates tikatenga tikakhazikutsa ma business athu.

21/11/2025

Kuti atabwereke ndalama amafuna tiwonetse kaye zinthu zoti ifeyo achinyamata kuno ku MALAWI tilibe or sindingwanitse kukhalanazo pakalipano

16/12/2024
09/12/2024

Who pays the President?

21/09/2024

It's very dangerous to have jealousy people around you. They look at you as a competition as you look at them as family or friends

18/09/2024

Osamazitengera kwambili zochitika zapano pa Facebook.

# Pa pa FB tili ndi anthu oti ma account awo akuwonesa kuti ndiophunzira kwambiri koma ndi classmate yemwe alibe in real life

# Pali anthu pano oti ma account owo akuonesa ali single koma anakwara ana kwatiwa.

# Tili ndi anthu pano pa FB oti amazangocheza nkhani zosiyanasiyana just to interact with friends koma sili life yawo

# Ena mazatula nkhawa zawo pano

Zambiri zikuchitika pa Facebook pano, Osamapupuluma ndi zapa Facebook!!!!!

06/09/2024

Iwowotu mtendere wawo umapezeka ngati inu mukulira
Anthu oyipa!!

05/09/2024

Just like sand in Hourglass, so are the days of our lives

04/09/2024

Feeling tired

Want your business to be the top-listed Government Service in Mzuzu?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Telephone

Website

Address

Mzuzu