Good morning Zomba
Eyes of Zomba
Eager to transform Zomba city.
16/08/2025
Akuti akapereka adyereni koma vote ndi mu mtima 😂😂😂
Achinyamata a ku Zomba nawonso ndi anthu. Adindo akungowagwiritsa ntchito pofuna ma vote basi. Akawina basi athana nawo.
Zomba youths, tisalore kugwiritsidwa ntchito ndi andalewa. Amatifuna pano, zikayenda athana nafe. Tiyeni tikane ziwawa.
Kodi muli mbali iti ya Zomba? Chonde musagulitse vote yanu, dzakavoteni mwa nzeru pa 16 September pano.
Ngati samatukula dera ali pampando nthawi yonseyi, asakunamizeni lero ndi tizitukuko tabodza. Achoke basi.
ma bus aulere akapezeka, kwerani. Ndalama zogawa zikapezeka, landirani. Koma inu chisankho chanu chikhale mumtima.
Nthawi yokwera ma bus aulere ija ikuyandikiratu 🤣🤣🤣🤣
Pano, Zomba community stadium yatsala pang'ono kudzadza pomwe anthu akusonkhana ku ma interview a DCSA. Zinthu sizilibwino.
Click here to claim your Sponsored Listing.
