LIFE IS A LONG JOURNEY
PART 1
CHONDE MUSANAYAMBE KUWELENGA NKHANIYI TIPANGENI FOLLOW Nyamata wa ntopola PGS KUTI MA PART OTSATILA MUWAPEZE MOSAVUTA NDIPO PANGANI SHARE KU MA GROUP NDI ANZANU OMWE AMAKONDA NKHANI NAWO AYITSATE NAWO OMWE MULI NAWO
Moyo ndi ulendo wautali⌠ndipo palibe amene amadziwa komwe udzamutengere.
Pa mudzi wina wotchedwa Chitedze, pafupi ndi mzinda wa Lilongwe, panali mnyamata wina dzina lake Kelvin Banda. Kelvin anali mwana wa zaka 18, wamtendere, wanzeru, koma moyo wake unali wodzaza ndi mavuto.
Ankakhala ndi amayi ake okha, dzina lake Agnes. Bambo ake anamwalira ali aangâono kwambiri, choncho moyo wonse unakhala pa mapewa a amayi ake.
Tsiku lililonse, Agnes ankadzuka m'mawa kwambiri kupita ku msika kukagulitsa tomato, masamba, ndi anyezi. Koma ndalama zimene ankapeza sizinkakwanira ngakhale kugula chakudya chokwanira.
Nthawi zina ankagona ndi njala.
Koma Kelvin⌠anali ndi loto lalikulu.
âOne day ndidzakhala successful⌠ndidzachotsa amayi anga mu umphawi, no matter what.â
Izi ankazibwereza nthawi zambiri, ngakhale moyo sunali kumumwetulira.
Moyo wa Kusukulu
Kelvin anali ku secondary school, Form 4. Anali mâmodzi mwa ophunzira abwino kwambiri pa sukulupo. Aphunzitsi ake ankakonda kwambiri chifukwa cha khama lake.
âKelvin is one of the best students we have,â anatero aphunzitsi ena tsiku lina.
Koma vuto lake linali limodziâschool fees.
Nthawi zambiri ankachotsedwa kusukulu chifukwa chosowa ndalama. Izi zinayamba kumuvuta kwambiri.
Tsiku lina, ali mkalasi akuphunzira, munthu wina anabwera kudzamupeza.
âKelvin Banda?â
âYes, sirâŚâ anayankha mwamantha.
âHead teacher akukufuna.â
Mtima wake unayamba kugunda kwambiri.
Atalowa mu office, head teacher anamuyangâana mozama.
âKelvin, you are a good student. But rules are rules. Popanda fees, you cannot continue.â
Kelvin anangokhala chete.
âGo home, and come back with fees.â
Mawuwo anamudula mtima.
Kupweteka kwa Mtima
Kelvin atatuluka kusukulu, anayenda yekha mpaka kunyumba. Sanalankhule ndi aliyense.
Atalowa mânyumba, anapeza amayi ake akuphika nsima ndi ndiwo za masamba.
âKelvin, wabwera msanga lero?â anafunsa amayi ake.
Kelvin sanayankhe nthawi yomweyo. Kenako anati mofooka:
âAmayi⌠andichotsa kusukulu.â
Amayi ake anasiya zomwe ankachita.
âChifukwa chiyani?â
âFeesâŚâ
Maso a amayi ake anayamba kudzaza ndi misozi.
âMwana wanga⌠ndakhala ndikuyesetsa, koma zinthu zikuvuta kwambiri.â
Nthawi imeneyo, Kelvin anamva ngati dziko lonse lagwa pa mapewa ake.
Koma sanalire.
Anangoti:
âItâs okay amayi⌠ndidzapeza njira.â
Chisankho Chosintha Moyo
Usiku womwewo, Kelvin sanagone.
Ankaganiza zambiriâŚ
âNgati ndikhala chonchi, sindidzafika kulikonse. Ndiyenera kuchita something.â
Mâmawa mwake, asanatuluke dzuwa, Kelvin anadzuka.
âUkupita kuti mwana wanga?â anafunsa amayi ake.
âKu town⌠ndikafune ntchito.â
Amayi ake anadabwa.
âKoma iwe ndi mwana sukuluâŚâ
Kelvin anangonena mwamphamvu:
âI need to fight for my future.â
Moyo wa Ku Town
Kelvin atafika ku town, moyo sunali wosavuta.
Anayamba kugwira ntchito yonyamula katundu ku msika. Anthu ankangomuitana:
âBoy! Bwera kuno!â
Ankanyamula matumba olemera, nthawi zina ankavutika kwambiri.
Nthawi zina anthu sankamulipira.
Nthawi zina ankachita manyazi.
Koma Kelvin sanasiye.
Tsiku lina, ali wotopa kwambiri, anakhala pansi pafupi ndi shop ina.
Munthu wina wovala bwino, ngati businessman, anamuona.
Anayandikira pafupi.
âWhatâs your name, young man?â
Kelvin anayankha mwaulemu:
âKelvin, sir.â
âWhy are you working this hard?â
Kelvin anayamba kufotokoza zonseâŚ
Za moyo wake, za sukulu, za amayi ake⌠ndi maloto ake.
Munthuyo anamuyangâana kwa nthawi yayitali, osanena chilichonse.
Kenako anati:
âHmm⌠I like your spirit.â
Kelvin anadabwa pangâono.
Munthuyo anatulutsa khadi mu pocket yake, namupatsa.
âCome see me tomorrow.â
Kelvin anayangâana khadiloâŚ
Dzinalo linali:
Mr. Richard Phiri â CEO
Mtima wake unayamba kugunda kwambiri.
âCEO??â
Anayangâana mmwamba, koma munthuyo anali atachoka kale.
Chiyambi cha Kusintha?
Kelvin anakhala pansi, akuyangâana khadilo.
âCould this be my chanceâŚ?â
Koma nthawi yomweyo, mantha anayamba kulowa.
âBwanji ngati ndi prank? Bwanji ngati zinthu zisinthe?â
Komabe, mumtima mwake munali chinthu chimodzi:
Chiyembekezo.
(To be continuedâŚ)Life is a Long Journey â Part 1
Moyo ndi ulendo wautali⌠ndipo palibe amene amadziwa komwe udzamutengere.
Pa mudzi wina wotchedwa Chitedze, pafupi ndi mzinda wa Lilongwe, panali mnyamata wina dzina lake Kelvin Banda. Kelvin anali mwana wa zaka 18, wamtendere, wanzeru, koma moyo wake unali wodzaza ndi mavuto.
Ankakhala ndi amayi ake okha, dzina lake Agnes. Bambo ake anamwalira ali aangâono kwambiri, choncho moyo wonse unakhala pa mapewa a amayi ake.
Tsiku lililonse, Agnes ankadzuka m'mawa kwambiri kupita ku msika kukagulitsa tomato, masamba, ndi anyezi. Koma ndalama zimene ankapeza sizinkakwanira ngakhale kugula chakudya chokwanira.
Nthawi zina ankagona ndi njala.
Koma Kelvin⌠anali ndi loto lalikulu.
âOne day ndidzakhala successful⌠ndidzachotsa amayi anga mu umphawi, no matter what.â
Izi ankazibwereza nthawi zambiri, ngakhale moyo sunali kumumwetulira.
Moyo wa Kusukulu
Kelvin anali ku secondary school, Form 4. Anali mâmodzi mwa ophunzira abwino kwambiri pa sukulupo. Aphunzitsi ake ankakonda kwambiri chifukwa cha khama lake.
âKelvin is one of the best students we have,â anatero aphunzitsi ena tsiku lina.
Koma vuto lake linali limodziâschool fees.
Nthawi zambiri ankachotsedwa kusukulu chifukwa chosowa ndalama. Izi zinayamba kumuvuta kwambiri.
Tsiku lina, ali mkalasi akuphunzira, munthu wina anabwera kudzamupeza.
âKelvin Banda?â
âYes, sirâŚâ anayankha mwamantha.
âHead teacher akukufuna.â
Mtima wake unayamba kugunda kwambiri.
Atalowa mu office, head teacher anamuyangâana mozama.
âKelvin, you are a good student. But rules are rules. Popanda fees, you cannot continue.â
Kelvin anangokhala chete.
âGo home, and come back with fees.â
Mawuwo anamudula mtima.
Kupweteka kwa Mtima
Kelvin atatuluka kusukulu, anayenda yekha mpaka kunyumba. Sanalankhule ndi aliyense.
Atalowa mânyumba, anapeza amayi ake akuphika nsima ndi ndiwo za masamba.
âKelvin, wabwera msanga lero?â anafunsa amayi ake.
Kelvin sanayankhe nthawi yomweyo. Kenako anati mofooka:
âAmayi⌠andichotsa kusukulu.â
Amayi ake anasiya zomwe ankachita.
âChifukwa chiyani?â
âFeesâŚâ
Maso a amayi ake anayamba kudzaza ndi misozi.
âMwana wanga⌠ndakhala ndikuyesetsa, koma zinthu zikuvuta kwambiri.â
Nthawi imeneyo, Kelvin anamva ngati dziko lonse lagwa pa mapewa ake.
Koma sanalire.
Anangoti:
âItâs okay amayi⌠ndidzapeza njira.â
Chisankho Chosintha Moyo
Usiku womwewo, Kelvin sanagone.
Ankaganiza zambiriâŚ
âNgati ndikhala chonchi, sindidzafika kulikonse. Ndiyenera kuchita something.â
Mâmawa mwake, asanatuluke dzuwa, Kelvin anadzuka.
âUkupita kuti mwana wanga?â anafunsa amayi ake.
âKu town⌠ndikafune ntchito.â
Amayi ake anadabwa.
âKoma iwe ndi mwana sukuluâŚâ
Kelvin anangonena mwamphamvu:
âI need to fight for my future.â
Moyo wa Ku Town
Kelvin atafika ku town, moyo sunali wosavuta.
Anayamba kugwira ntchito yonyamula katundu ku msika. Anthu ankangomuitana:
âBoy! Bwera kuno!â
Ankanyamula matumba olemera, nthawi zina ankavutika kwambiri.
Nthawi zina anthu sankamulipira.
Nthawi zina ankachita manyazi.
Koma Kelvin sanasiye.
Tsiku lina, ali wotopa kwambiri, anakhala pansi pafupi ndi shop ina.
Munthu wina wovala bwino, ngati businessman, anamuona.
Anayandikira pafupi.
âWhatâs your name, young man?â
Kelvin anayankha mwaulemu:
âKelvin, sir.â
âWhy are you working this hard?â
Kelvin anayamba kufotokoza zonseâŚ
Za moyo wake, za sukulu, za amayi ake⌠ndi maloto ake.
Munthuyo anamuyangâana kwa nthawi yayitali, osanena chilichonse.
Kenako anati:
âHmm⌠I like your spirit.â
Kelvin anadabwa pangâono.
Munthuyo anatulutsa khadi mu pocket yake, namupatsa.
âCome see me tomorrow.â
Kelvin anayangâana khadiloâŚ
Dzinalo linali:
Mr. Richard Phiri â CEO
Mtima wake unayamba kugunda kwambiri.
âCEO??â
Anayangâana mmwamba, koma munthuyo anali atachoka kale.
Chiyambi cha Kusintha?
Kelvin anakhala pansi, akuyangâana khadilo.
âCould this be my chanceâŚ?â
Koma nthawi yomweyo, mantha anayamba kulowa.
âBwanji ngati ndi prank? Bwanji ngati zinthu zisinthe?â
Komabe, mumtima mwake munali chinthu chimodzi:
Chiyembekezo.
(To be continuedâŚ)
Tabwelaso tiyese nawo tili ndi group pa wapp ngati mukulifuna tihaleni pa +258862702022 or kulowa kudzela mu link ili mu coment box mu
APATSENI ANZANU AWELENGE NAWO
Nyamata wa ntopola PGS
Welcome to my library đđ
For business or WhatsApp, my number is... +258862702022
TWIN BROTHER
[GOOD AND BAD]
LIKE AND SHARE FOLLOW MY PAGE Nyamata wa ntopola PGS
PART 2
CONT...
Mike anali mu class pamene bro wake anapita ku mowa ndi anzake
Nthawi yoweluka itakwana jorge anaweluka ananyamuka ulendo wa ku nyumba ali mu njila anakumana ndi brother wake pa njila
Mike:ok ndimadikila iweyo tiyeko
Jorge: mudzitelo kani
Mike: ndataniso kodi
Jorge: kani mudzingobwelera pa njila osakafika ku school
Mike:wakuuza ndani kuti sindinakafike ku xool mesa achita kundibweza kuti ndachedwa
Jorge: koma ine ndakudzutsa iwe makani simumafuna kale kupita ku xool mumafuna kupita ku mowa ko
Mike: nkhani ithele p***a ikakangofika ku deni ndikakuponda
2 WEKS LATER
Mike amapitilizabe kumajomba ku school koma jorge amalimbikila kuti akhoze ndipo anthu anapitilizabe kumukonda jorge
New story new day new negbor
Mike ndi jorge atangokhala pa khonde anaona galimoto lomwe linaima pafupi ndi nyumba yawo ndipo munatuluka nkazi koma anali owoneka bwino kwambili ndipo atatsika galimoto anabwela pa fupi pamene panali anchina mike ndipo anafunsa
Pepani pokusokonezani
Mike: aiso sunatisokoneze
Anayankha mwachangu poti anali atadyelela maso
Chabwino Kodi kwa achalamanda ndimbali ya kuno
Jorge:eya mwafika ndi uko
Anatel jorge ukuAkumulozela
Mike: aaah iwe munthu wachoka kutali udzimulozelaso tiyeko ndikupelekeze
Ndipo mike ndi nkazi uja ananyamuka ndipo mu njila mike amafunitsitsa atamudziwa nkazi uja koma zimamuvuta kufusa mpaka anafika kumene amapita
Zikomo mwandithandiza achimwene
Anatelo nkazi uja
Mike:osadanda
Mpaka mike anabwelera koma ali osangalala ngati walandila salary mwezi usanathe
Patatha masiku awili mike anali odabwa kuti nkaz uja akumapita ku school ndi jorge ndipo mike anali ndi kwiyo kwambili ndipo amangofuna atangomupha chifukwa nkaziyo anali owala kwambili
CONT.....
my number +258862702022
APATSENI ANZANU AWELENGE NAWO
TWIN BROTHERS
[GOOD AND BAD]
FOLLOW MY PAGE Nyamata wa ntopola PGS
PART 1
LIKE AND SHARE
Eh tivayeso pa geli eeeh ai km yatopetsa
Koma man inuyo school tangophuzila kwa tho weks bs mwatopa nayo
ngat umakonda kuphuzila ndi wekha ine ai zilibe tsogolo izi
brow tsogolo silidziwika tiyen tingogela bs
Uku kunali kucheza kwa mike ndi twin brother wakwe jorge atawadzutsa makolo kuti apite ku school iwowa ali from 2 pa ulongue secondary school ndipo amaphuzila class rom imodzi koma mike amadana kwambili ndi mbale wake iye amaganiza kuti anthu amakonda kwambili mbale wake ndipo amakhala ndi nsanje amamuchitila zoipa koma jorge amayesetsa kt Brother wakeyo asamamude koma ai
PRESENT DAY
Jorge: brow tiyeni pa geli
Mike: iiii ase panga zako ukanika kumapita cha ine mesa ati ndiwe wanzelu panga nzelu zakozo ndisiye mixeew
Anatelo kucheza kwawo ndipo jorge anangokozeka kupita ku xool ndipo a mike amangogona ndipo anachedwa kwambili popita ku xool
Ananyamuka mochedwa ku xool anangofika pa gate kupeza kuti ochedwa akubweza ndipo panja pomwepo anakumana ndi anzake osokonekela ndipo anatengana ulendo okamwa mowa ku nalo ena kuiwala za xool
ndipo jorge anali biz kuphunzila mu class mwake
SPONSOR MY NUMBER +258862702022
APATSENI ANZANU AWELENGE NAWO
ndabweraso guys tiyambeso nkhani ma guys ndipangeni follow
19/02/2026
*âď¸âď¸NDINAFERA MAWANGAâď¸âď¸*
```PART 1```
*đ°đ°By Mr* ```Malack Maksy Asuba```
*FOLLOW US ON FACEBOOK PAGE..........* Maksy Asuba Stories
*WHATSAPP GROUP.............*
0634735482
```SPONSORED BY.........
```
Elias Hamzy
Owen Kankono
Moyo Kunyenga
Loveness Nyabanda
...........................................
...........................................
Kunali chakumazuro pomwe ndimachokera kotunga madzi inde kudendekera chidebe ndithu........ndinali ndikuyimba kamuluzu angakhale kuti inenso sindimaziwa kuti ndinyimbo yanji yomwe ndimayimbayo koma kunena zoona inali nyimbo yodandaulisa motengera ndimoyo omwe ndimadusamo ine.
Ndinali ndikuyenda ndimawu asokonombwe oti pang'ono pang'ono wangawu ndithudi ndikafika komwe ndikupitaku......
Izi zinali chomwecho kamba koti ndinali ndimimba yamiyezi 7 moti ndingayimbilamo kuvina kwake kunali kusisita mimbayo moti ndimamva kukoma ndikamayimba zosamvesesekazo.
Ndinayima njiiii nditayandikila kunyumba kwanga pomwe kunali mkangano owopsa oti mkuchosanapo chimbenene
Lero tu akusamuka ndipo akamachoka komwe wapitako mumuonese nyangwita zake azipita........
Awa ndimawu omwe ndinamva koma poti inenso ndinali munthu obalarika sinathe kuwatolera kuti amalankhulayo ndindani nanga yemwe akuyenera kutenga nyangwita zake ndindani, zomwe zinapangisa kuti ndiyende mwachangu sopano koma mozikakamiza motengera ndimene ndinaliri munthune.
Chabwino ngati mukukana zimenezo ingoyembekezerani nonse kusamuka pamudzi.......ndinamvaso mawu ena omwe kwa ine zinali ngati ndikuponda clutch ndikuzafinya giya fiiii kuti galimoto iyende mwachangu koma mimba ndiyo imamanga mabuleki.
Nde funso nkumati akudandaulayu ndani??.........nanga yemwe akuyenera kusamukayo ndani??...........
Zikuoneseratu kuti tangoyambila posayambila ndeno inu onesani kuyikonda kuti tisokole nkhani yonse pondipanga sponsor kuti nkhani izibwera mwachangu komanso zimathandiza kupeza mayina amunkhanimo........
M***a kundiyimbila kapena kundihala ku wasapu pa 0634735482
LOVE IS IMPOSSIBLE
FOLLOW MY PAGE Nyamata wa ntopola PGS
PART 3
Recap ya Part 2:
Tawanda anayamba kugwirizana ndi Melissa, koma panali vuto: Tawanda ankayamba kukondanso wina â a quiet girl named Grace, yemwe ankakhala mâkalasi limodzi ndi iwo. Melissa anali kuyamba kuona kusintha pa Tawanda, koma sanadziwe kuti chinsinsi chachikulu chinali chikubisidwa.
---
PART 3: Confused Hearts
Mâmawa wa Lachitatu, nyengo inali yabwino kwambiri ku sukulu ya St. Lawrence Secondary School. Mbalame zinkaimba panja, koma m'mtima mwa Melissa, zinali zosiyana. Ankakhala pa bench ya mâbwalo atangofika kusukulu, akuyangâana mmwamba ngati kuti akufuna thandizo kuchokera kumwamba.
"Tawanda akusanduka," anangonena mâmtima mwake. "Why is he so distant lately?"
Iye anamutumizira message usiku watha:
> âHey, hope youâre good. You were quiet today. Did I do something wrong?â
Koma Tawanda sanayankhe. Koma chowonadi nâchakuti, Tawanda anali pansi pa chisokonezo cha mtima.
Iye anali atakhala pa study table yake usiku umenewo, akuganiza:
> "Why am I thinking about Grace? Ndi Melissa yemwe andithandiza ku campus life, koma mtima wanga ukuponda ku Grace."
Grace anali mwana osiyanasiyana ndi Melissa. Iye sankalankhula zambiri, koma nthawi zonse anali wokoma mtima, wopatsa ulemu, komanso wozikika. Nthawi zambiri ankakhala okha, nthawi zina ku library, akulemba zolemba kapena kuwerenga mabuku a psychology.
Tawanda anayamba kupeza njira zopita ku library nthawi zambiri, komanso samachita kuvala ma uniform bwino, something that only Grace ankamunena:
> âYour tie is too loose, Tawanda. Fix it,â anamuuza tsiku lina, ndi smile yofatsa.
âOoh, ndiye muli discipline prefect pano?â Tawanda anayankha, akuseka.
âNo. Just someone who hates disorder,â Grace anayankha, akuchokapo.
Zinthu zinkayamba kusintha.
---
Melissa anayamba kuzindikira kuti nthawi zambiri Tawanda sangayankhe ma messages mwachangu. Iye amamupeza akuseka ndi Grace, nthawi zina akuchita projects mâmakalasi omwe sakanali nawo.
Tsiku lina, pa Friday, ana onse a Form 4 analembedwa kuti akhale pa group assignments. Surprisingly, Tawanda analowa mu group imodzi ndi Grace, osati ya Melissa.
Izi zinamupweteka Melissa, koma anangopanga poseka.
> âSo, you joined their group? I thought weâd work together,â adafunsa Melissa.
âEeeh, sorry Mel, inakakamizidwa... you know how Mr. Banda is,â Tawanda anayankha.
âHmm, okay,â iye anayankha, koma mâmtima: âWhy didnât he fight to be in my group?â
---
Weekend ya Boarders
Tsiku la Loweruka, sukulu inachita âTalent Showâ ku hall. Ana ambiri ankachita rap, kukamba nthano, kapena kuimba. Grace sanali wotchuka pa izi, koma nthawi ina, anyamata a Form 3 anapempha volunteer kuti aziwawerengera poem yolembedwa mu French. Palibe amene anadzuka.
Koma nthawi yomweyo, Grace anayimuka, ndipo anapita kutsogolo. Ataimika mic, anawerenga:
> âLâamour ne demande pas la perfection, juste la prĂŠsence sincèreâŚâ
(âLove doesnât ask for perfection, only genuine presence.â)
Anamaliza ndi kalankhula kochepa, then anapuma mwakachetechete.
Tawanda anali atangowomba mâmanja atachita speech ya Grace. Sheâs not just smart, sheâs special, anaganiza. Ndipo nthawi yomweyo, Melissa ankayangâana Tawanda.
She saw something different in his eyes.
âThat look⌠he never gave me that look,â anaganiza.
---
Late Night Talk
Usiku wa Lamlungu, Melissa anatuma voice note kwa Tawanda:
> âTawanda, I feel like Iâm losing you. Maybe Iâm just overthinking, but I miss how we used to talk⌠If thereâs something I should know, please tell me.â
Tawanda anasunga voicenote, osayankha nthawi yomweyo.
Iye anayangâana ceiling ya dorm ya Form 4 boys, ndipo anachita regret.
> âKodi ndamupweteka Melissa? Nanga bwanji ndikumva ngati Grace ndiye yemwe mtima wanga ukukonda tsopano?â
Anatsuka maso, natuluka panja. Dzuwa linali kutuluka pangâono.
---
Monday Morning Decision
Tawandayo sanamve bwino. Iye ankafuna kulankhula ndi Melissa, koma nthawi yomweyo, Grace anamubwelera pakhomo la class ndi textbook yomwe Tawanda anaiwala.
> âI saw this at the library,â Grace anamuuzira.
âAhh, thanks⌠You didnât have to,â Tawanda anayankha.
âWell⌠maybe I wanted to.â Grace anaseka, kenako anachoka.
Pamene Tawanda ankayangâana mmwamba, sanazindikire kuti Melissa ankamuonera kuchokera pa window ya corridor.
Maso ake anali odzaza ndi madzi.
---
To Be ContinuedâŚ
Mu Part 4:
Will Melissa confront Grace? Kodi Tawanda adzaganiza chiyani? The love triangle is getting more complicated, ndipo moyo wa pa sukulu ukupita patsogolo ndi ma test, jealousy, secrets⌠and heartbreak.
---
Hehehe hulu nayoni ... Wapp number+258862702022
APATSENI ANZANU AWELENGE NAWO
LOVE IS IMPOSSIBLE
FOLLOW my page Nyamata wa ntopola PGS
Wapp or sponsor+258862702022
â PART 2:
Mwezi wa October unalowa, ndi mphepo yaku Zomba yomwe imakupha mosakwiya.
Tawanda anali mâchipinda chake cha Hall 2, akungoyangâana pa ceiling ngati munthu opanda chiyembekezo. Foni yake inali pa silent, koma nthawi ndi nthawi ankayiyangâana. Palibe text kuchokera kwa Melissa. Palibe chilichonse kuchokera kwa aliyense amene ankadziwa za kupweteka kwake.
Melissa anali busy â busy kukhala wokondwa ndi Brian.
> "Ndiye chonchi chikondi chimakhala?"
Anangonena Tawanda pamene amaika notebook pansi.
Analephera kugona usiku wathunthu. Mâmutu mwake munali mawu omwe Melissa analankhula:
> "You're like a brother to me..."
"Brian and I... we're kind of seeing each other."
Iye sanamvetse. Sanamufunsire banja. Sanapemphere moyo wake. Iye anali ndi chikondi choona â koma tsopano chikondicho chinali chowawa.
---
Madzi a Mtima ndi Madzi a Misozi
Kumasiku, Tawanda anayamba kupweteka kwambiri pa campus. Ena anayamba kunyoza:
> "Uyu ndiye uja anapempha Melissa, koma anangomulowetsa pa friend zone!"
"Umunthu opanda ndalama umenewo ndi umene umayambitsa ma 'brother'..."
Ma boys ena ankamucheka, ena ankamuseka, koma iye samaletsa mtima. Sanayankhule, koma mkati mwa iye, panali moto waukulu. Moto wokhumudwa. Koma osati wofooka.
Anayamba kulemba nthawi iliyonse akumva pain. Anaika mawu ake mu notebook yotchedwa âMoyo Wopanda Iweâ.
---
Kusintha kwa Njira: Campus Life Yamuyamba
Mu class, Tawanda anayamba kukhala wokhazikika. Anakumana ndi lecturer wina wa literature dzina lake Mrs. Phiri amene anali okondwa kwambiri ndi mmene amalemba.
> "Tawanda, your short story about heartbreak... itâs powerful. You have a gift."
Aphunzitsi ena anayamba kuzindikira kuti mnyamatayu ngakhale akakhala chete, ali ndi luso lolembalemba lodabwitsa.
Ndiye tsiku lina ku campus cafeteria, anaima ku line akudikirira nsima ndi beans, ndipo panali mtsikana wina kumbuyo kwake, wokongola, wosavuta kulankhula naye.
> "Excuse me, is this line even moving?"
> "Haha, slowly like broken hearts," anayankha Tawanda.
> "Haha! Broken hearts? You sound like a poet!"
> "Maybe I am," Tawanda anangonena, osadziwa kuti uja ndiye unali mwayi watsopano wa moyo wake.
Dzina la mtsikanayu anali Chikondi.
---
Chikondi: Mkazi Watsopano Wamoyo Wake
Chikondi anali mtsikana amene sanadzionetsetse. Sanadzitukumule. Sanavale zodula, koma mawonekedwe ake anali a mkazi wa nzeru. Amachokera ku Neno, ndipo anali mâfirst year, ngati Tawanda.
Anali mâFaculty of Education.
Zinthu zidayamba kukhala zosiyana.
Pamene Melissa ankangoyenda ndi Brian, kusangalala pa ma parties, Tawanda ankangokhalira kuphunzira ndi Chikondi. Ankakhala nthawi zambiri pa library, pamalo opanda phokoso, akugawana zinthu za moyo wawo.
> "What do you write about mostly?"
"Zinthu zomwe anthu sakufuna kumva. Zomwe zimapweteka."
"Umm... ndiye maybe ndiyenera kukuthandiza kulemba zinthu zosapweteka."
Tawanda anayamba kuseka. Sese yomwe sanachite kwa milungu yambiri.
---
Melissa: Kuzindikira... Koma Too Late
Ndiye tsiku lina, Melissa anali pa class ya communication, ndipo lecturer anapempha ophunzira kuti awerenge zolemba zomwe zinapambana mu kampeni ya creative writing competition.
Dzina lotchulidwa linali Tawanda Mvula.
Mutu wa ntchito yake unali âNdinalira Nthawi Yoti Umasekeâ.
Pamene lecturer ankawerenga ndime za nkhaniyo, Melissa anatseka maso. Maonekedwe a mawuwo anali a moyo wake.
> "Ndinaona maso ako akamaseka naye, koma ndimadziwa kuti maso amenewo anali anga. Ndinaona manja ako akamugwira, koma ndi ine amene ndinalemba dzina lako mu mtima..."
Melissa anasokonezeka. Anakumbukira nthawi imene Tawanda anali naye pafupi, amamulembera ma poem, amamugulira chips pa night study, ngakhale sanali ndi zambiri.
Pamene class inatha, Melissa anaimira kunja kwa hall, akucheza ndi Brian, koma maso ake anali kufunafuna Tawanda.
Brian ankangolankhula za ma sneakers a ku UK. Za TikTok. Za Benz yomwe bambo ake angamugulire. Koma Melissa sankamumvetsera.
> "Hey, are you okay?"
"Yeah, I'm fine. Just tired..."
Koma mkati? Sanali fine.
---
Tawanda Watsopano, Moyo Watsopano
Tawanda anayamba kulengezedwa pa campus. Anthu anayamba kumukonda chifukwa cha zolemba zake. Iye ndi Chikondi anapanga page ya Instagram yotchedwa âZolemba za Mtimaâ â ndipo ma likes anali kukwera.
Amayamba kulandira ma invite oti apereke ma talk pa ma events. Campus inazindikira kuti mnyamatayu sanali wamba.
Tsiku lina, Melissa anamutumizira text:
> âCan we talk?â
Tawanda anaiona. Anatseka foni. Anayangâana ku Chikondi amene anali atagona pa bed, atamugwirira dzanja usiku.
Anangomwetulira pang'ono.
> "Sometimes, pain is a gift... chifukwa imatsegula khomo la choonadi."
Ananena mâmutu.
APATSENI ANZANU AWELENGE NAWO
12/12/2025
ngati mumakonda nkhani zanga lembani Kuti pitiliza akangokwana anthu 5 olemba Kuti ndimakonda ma story ako pompo ndiyamba kuponya nkhani đĽşâď¸âď¸âď¸ Ndili ku ma coment đđ
tadzukaso ndi moyo ai mulungu ndingoti zikomo â¤ď¸â¤ď¸â¤ď¸đđ
LOVE IS IMPOSSIBLE
Follow my page Nyamata wa ntopola PGS
PART 1: First Day, First Crush
Zomba. Chancellor College. September, nthawi yOtentha ikuyamba.
Timaona galimoto ikulowa pa gate. Idzaza ndi ana a sukulu okondwera, ena odekha, ena osadziwa chimene akuyembekezera. University yatsopano, moyo watsopano, ndi anthu atsopano.
Tawanda anatsika pa minibus ya ku Blantyre, atanyamula bag lake lamâmwamba. Anayenda pangâonopangâono, akuyangâana kumanzere ndi kumanja. Koma ku mtima kwake kuli zinthu zambiri: mantha, chisangalalo, komanso chikhumbo chachikulu chokhazikika.
> "So this is Chanco... the place everyone says âyou find lifeâ."
Ananena choncho mumtima, akuyenda molowera ku Hall 2, komwe amapatsidwa ma room.
Tawanda sanali mwana wa mâdziko la ndalama. Amachokera ku Chirimba, Blantyre. Abambo ake anali wogulitsa masikelo a tomato ku Limbe Market. Mayi ake anamwalira ali Form 2. Tawanda anadutsa zovuta zambiri kuti afike kuno: kugulitsa zitumbuwa, kuphunzira ndi nyali, komanso kupanga zinthu zomwe ena amangomva ngati nthano.
Atangofika ku Hall, anaona abale ambiri ali busy: ena akulankhula English yokakamira, ena ali ndi ma laptop a pansi, ena akuseka ngati amadziwana kale.
> "Bro, mukufuna ndithandize kusenza bag?"
Wina anafunsa Tawanda.
> "Ayi, ndiyenela basi. Zikomo."
Anayankha Tawanda, mwaulemu.
Koma mâkati kuli mantha. Anali ndi self-doubt:
"Kodi ndidzatha kukondedwa ndi munthu wina kuno? Kodi ndidzapambana pa sukulu? Kodi ndidzapeza bwenzi?"
Kuyamba kwa Maphunziro
Mâmawa wa Lachitatu, Tawanda anapita ku lecture hall kukakhala pa orientation. A Philosophy lecturer amene amatchedwa Dr. Mbewe anali atavala suit ya blue, akulankhula zinthu za moral reasoning.
Pamene Tawanda akuyesera kutsatira, anaona mtsikana wolimba mtima, wokongola kwambiri, wovala chitenje chachikasu ndi top yofiyira. Mtsikanayu anakhala pafupi naye, koma osamuyang'ana.
> "Sorry, is this seat taken?"
Mtsikanayo anafunsa.
> "No... I mean yes... I mean, it's free!"
Tawanda anayankha atayiwala kulankhula bwino.
Mtsikanayo anaseka pang'ono, kenako anakhalako.
> "I'm Melissa. And you?"
"T-Tawanda."
"Nice to meet you, Tawanda."
Pamene lecturer akupitiriza kulankhula za Plato, moyo wa Tawanda udayamba kusintha. Zinali ngati nthawi yayima. Melissa anaseka nthawi ina akumva lecturer akulemba âethicsâ paboard. Kumasekawo kunawoneka ngati nyimbo. Chibwibwi!
Chikondi Choyamba? Kapena Masewera?
Mâmawa wina, Tawanda anakumana ndi Melissa ku library.
> "You again?"
Melissa anaseka.
> "Looks like fate loves me."
Tawanda anaziyankhira, pamene mtima wake ukufinya kwambiri.
Anakhala pamodzi pa table, nâkumayamba kuphunzira. Koma panali ma silence a chisomo pakati pawo. Melissa anali mwana wa mabwana â abambo ake ndi diplomat ku Germany. Anabwera ku Malawi kuti apunzire kwawo, koma moyo wake anazolowera kukhala wa standard yokwera kwambiri.
Tawanda, ngakhale sanawauze, ankazindikira kuti iye ndi Melissa adachokera ku ma world osiyana.
> "So, what do you want to do after college?"
Melissa anafunsa.
> "Ndikufuna kukhala journalist, or maybe author. I love writing."
"Wow. I think you'd be good at that. You speak with your eyes, not your mouth."
Melissa ananena izi atayangâana maso a Tawanda. Tawanda anangoseka pangâono, koma mkati mwa iye munali chipolopolo cha mtima.
Koma nthawi yinkadutsa. Masiku atatu pambuyo pake, Tawanda anaona Melissa akuyenda ndi mnyamata wina wovala ma sneakers a ku UK, akumwetulira.
> "Who's that guy?"
"Oh, that's Brian. Heâs my cousin. But why do you look jealous?"
"No, no... I was just... never mind."
Koma kuchokera pa nthawi imeneyo, Brian anakhala pafupi kwambiri ndi Melissa. Nthawi zina, Melissa samayankha ma text a Tawanda. Koma Tawanda sanaleke kuyesa. Iye ankafuna kusonyeza kuti ngakhale alibe ndalama, chikondi chake chinali chenicheni.
Gawo Lopweteka: Kumva Chabwino pa Zowona
Sabata imodzi yatha. Pa Friday night, Tawanda analandira voicemail kuchokera kwa Melissa:
> "Hey Tawanda... um, I think you're really sweet. But you're like a brother to me. I just wanted to be honest. Brian and I... well, weâre kind of seeing each other now. I hope you understand."
Tawanda anangokhala chete. Kanthawi. Nthawi ina, analira. Osati chifukwa choti sanamufune, koma chifukwa choti moyo unkamuuzanso zomwe anazolowera: zabwino sizimakhala zake.
> "Love is impossible, huh?"
Ananena, atangotseka foni.
Pamene nyimbo ya John Legend â All of Me ikuimbidwa mâchipinda cha mnzake, Tawanda anayangâana pa ceiling. Ndiye ananyamuka, anatenga notebook yake, ndipo anayamba kulemba.
âMaybe if love is impossible for me, Iâll write it for others.â
---
Support Wapp number +258862702022
APATSENI ANZANU AWELENGE NAWO
tipitilize kapena tiyambe ina đ¤đ¤ coz ma like akuchepa đĽşđĽş
