Ulimimbikire school udzakhale pabwino mwana wanga lero tikukatenga katapira kwa anthu osaphunzira mmmmmm koma dziko ili kaya inakhala bwanj kaya
Ronex Diva
Grocery Management
Mudzingondimvetsetsa kuti ndimakhala buyz
Mundipange block then unblock koma anthu Inu muli ndinthawi yosewelesa kwambir et?
Best wishies for all form four students as you going to attend the final examination tommorrow, let's ask a God to safe gaurd you all the time
08/08/2022
😂😂😂😂
❤
31/07/2022
Buy me airtime/data and send me transport money" is the first sign of a useless girlfriend.
Akuti zoti anagwirizana 5 years wina alamulire kenako 5 years inayo winaso alamulire zimenezo sakudziwa ndipo kuchimpani kwawo kulibe gwirizano umenewo mmmmmm mfana oganiza boh zikukumvekera motan?
Ulendo wapabwato satsitsirana pakati pa njira ayi 🤔🤔🤔🤔🤔🤔
Olakwa ndan chakwera,global issues kapena ovota Ife?
Click here to claim your Sponsored Listing.
Location
Category
Contact the business
Website
Address
Nchalo
Blantyre
