Ma guys inunso ngat muli nazo nkhani kuma ponya
Nkhani ZA KWA Safalao
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Nkhani ZA KWA Safalao, Public & Government Service, Blantyre.
Kwa amene timamumu dziwa Andrew mwale watisiya dzulo usiku atagwidwa ndi shock
Gyz nkhani yachison yango tipeza kumene nyamata amene atchuka kt NYANI koma dzina lake la nchik*ta ndi wiladi wa tisiya.
Gooooooooo 4-0 kkkkkkkk neba apsye mtima BB WOYEEEEEEEEEEEEH
kod gyz ndizoona k*t munthu ukafuna kukumba chimbuzi uzikadzisa amfumu?
Tsikana wina wa kwasafalao dzina lake zeffa watisia dzana.may her soul rest in peace
Atsikana ena odziwika bwino aphophola m'mawa wa lero pa nsika wa safalao chifukwa chot ana bwekana zuvala nde wina pokumbusa mbasha zake panali kusanvana ayambapo kuithana khonya.Mau awiri kwa atsikana amenewa.
Click here to claim your Sponsored Listing.
Location
Category
Telephone
Website
Address
Blantyre
