mwapanga maplan otani a khrisimasi? pakufunika kupanga ziganizo zanzelu,chifukwa nthawiyi ena amaluza miyoyo,tisangalale mosamala
Lupafya,Kasungu
your trusted source of activities taking place in lupafya and sorrounding areas
Abale Ndi Alongo,mwadzuka Bwanji?Sikupambana Kwanga Kapena Kwanu Kuti Tiwone Tsiku Lalelo, Mwadzuka Ndi Moyo Lelo, Lembani !
28/08/2015
Manja Mukuwaonawo Ndi A Awasili Ndi Anzao Atamangidwa Ndi Apolice Kamba Kopopa Mafuta Kushayona,moti Tikunena Pano Anthuwa Ali Ku Lilongwe Ku Headoffice Ya Shayona!
Chikhamu wamenyedwa lachinayi lapitali kamba kamatama omwe amapanga atalanda vikitolia mkazi wa more news to come...wanna keep u updated!
DZULO KUNALI NDEU MMUDZI MWA CHIMDIDI POMWE MWANA WA CHINKHWASALE/AFUMU A KAPENA K*T A YOLAMU NDI A AMACHOTSANA CHIMBENENE,ANTHUWA ANAMENYANA KAMBA KOLIMBILANA [OWNERSHIP] UMWINI WA MALO APANYUMBA YA A MAKILOYD. CHATSITSA DZAYE K*T NJOVU ITHYOKE MNYANGA NDICHAK*T YEMWE NDIMUPHWA WA A MASEYA ANAKAMANGA KACHISAKASA MMBALI MWANSEU NDICHOLINGA CHOMAMETELAMO ZOMWE ZINAKWIYITSA KHWAULE NGATI AMANGA PANYUMBA PAKE,ETI POT FUMU NDIIYE NDIPO AMAFUNA AKANAPEZA IWOWO K*TI ALANDEPO ZAMMANJA.ZINALI ZOSEKETSA CHIFUKWA MAKILOYIDI ATAKWIYA ANAKALOWA MNYUMBA NDIKUKAVALA ETI YOTI APONDERE NAYO FUMU KWHAULE KOMA MMALO MWANA ANAYAMBA K*TENGA MITENGO NDI NJERWA ETI KUOPA CHIKWANJE CHOMWE CHINALI NDI A KHWAULE! ine admin wanu
Bambo Wina Yemwe Mkazi Wake Wamkulu Adamuotchela Zovala Walilila Kuutsi Mkazi Wamng'ono Atamuotchela Fodya Yese Oti Akadakwana Mabelo 22,mamunayu Anakanitsitsa Kuti Mkaziyu Amangidwe Poti Ali Ndimwana Wamng'ono Komanso Panalibe Chomwe Akanapindula Pakumangidwa Kwake,panopa Mkazi Wamng'onoyu Ali Kwao Pomwe Akuti Sasiya Vikitoria Yemwe Ndi Mkaz Wamkulu Wamwamunayu mpaka Atamukwatira Basi!
Lupafya Health Centre ikusoweka doctor kamba kamafumu odzikonda omwe azungulira chipatalachi,zomwe zapangitsa kuti anthu avutike kwambiri,kumaenda mtunda wautali kufuna thandizo lamankhwala. ABALE ANGA TIENI TIKONDE DERA LATHU,KUPANDA K*TERO SILIDZATUKUKA MPAKA KALE,shame on foolish chiefs who chased away a doctor!
19/01/2015
akaz kumenyana kamba kamwamuna,mkaz mukuona wavala zamizele yakudayo ndie wamenyewa,zachitika posachedwapa kwachimdidi
Click here to claim your Sponsored Listing.
Location
Category
Website
Address
Mtunthama-shayona Road From Kasungu Town
Kasungu
