28/10/2026
𝐀𝐍𝐓𝐇𝐔 𝐎𝐊𝐖𝐈𝐘𝐀 𝐀𝐊𝐔𝐏𝐇𝐖𝐀𝐍𝐘𝐀 𝐎𝐅𝐅𝐈𝐂𝐄 𝐘𝐀 𝐈𝐌𝐌𝐈𝐆𝐑𝐀𝐓𝐈𝐎𝐍 𝐊𝐔 𝐋𝐈𝐋𝐎𝐍𝐆𝐖𝐄, 𝐊𝐀𝐀𝐌𝐁𝐀 𝐊𝐎𝐋𝐄𝐏𝐇𝐄𝐑𝐀 𝐊𝐔𝐏𝐄𝐑𝐄𝐊𝐀 𝐌𝐀 𝐏𝐀𝐒𝐒𝐏𝐎𝐑𝐓
Anthu ochuluka amene analipira Ndalama zama Passport ku Lilongwe, akuthamangitsana ndi a Police pa Office ya Immigration.
Izi zadza kaamba kakulephera kwa office ya Immigration kupereka ziphazozi kwa anthu