Malawi wanga

Directions Website Contact the organization

Malawi wanga This is the Entertainment Arm of .Trending updates on malawian celebrities,Entertainment,News and many more
✔️ Follow
✔️Like
✔️Share
(4)

Goodnight Pa Mudzi pano 😋😋
19/10/2026

Goodnight Pa Mudzi pano 😋😋

19/10/2026

Ukakhala mchikondi chokakamiza💔 umakhala kapolo
ukati Bea ndakusowa♥️
iye amvekele...??

19/10/2026

Kupatula ntendele wamuntima uliposo ntendele wina ngat😄🏌️

why this picture is trending??
19/10/2026

why this picture is trending??

Very Sad : Anthu pa Kanengo adzukila chisoni pamene Wanjinga amene amathawa police ndi zigubu za mafuta anagwa, mafuta k...
19/10/2026

Very Sad : Anthu pa Kanengo adzukila chisoni pamene Wanjinga amene amathawa police ndi zigubu za mafuta anagwa, mafuta kuyaka iye ndi njinga zonse kupsa. Ma report akutelo

May His Soul Rest in Peace & May God comfort all family and friends 🕊️

18/10/2026

📌 ⚽⚖️🏆𝗙𝗗𝗛 𝗕𝗔𝗡𝗞 𝗣𝗥𝗘𝗠𝗜𝗘𝗥𝗦𝗛𝗜𝗣 𝗧𝗢𝗗𝗔𝗬 𝗥𝗘𝗦𝗨𝗟𝗧𝗦

🚩 𝗙𝗗𝗛 𝗕𝗔𝗡𝗞 𝗣𝗥𝗘𝗠𝗜𝗘𝗥𝗦𝗛𝗜𝗣 𝗟𝗜𝗩𝗘 𝗨𝗣𝗗𝗔𝗧𝗘

𝗠𝗮𝗳𝗰𝗼 0️⃣➖3️⃣ 𝗕𝘂𝗹𝗹𝗲𝘁𝘀 (𝗖𝗹𝗮𝘃𝗲𝗿 𝗸𝗮𝗹𝗮𝗺𝗯𝗼 ⚽, 𝗧𝗶𝗻𝗮𝘆𝗲 T𝘀𝗶𝗺𝗯𝗮 ⚽⚽)
𝗥𝗲𝗱 𝗹𝗶𝗼𝗻𝘀 0️⃣➖0️⃣ 𝗘𝗸𝗵𝗮𝘆𝗮
𝗕𝗹𝘂𝗲 𝗲𝗮𝗴𝗹𝗲𝘀3️⃣➖0️⃣ 𝗖𝗵𝗶𝘁𝗶𝗽𝗮 (𝗧𝗼𝗻𝗶𝗰𝗸 V𝗶𝘆𝘂𝘆𝘂 ⚽⚽, 𝗪𝗲𝗯𝘀𝘁𝗲𝗿 𝗺𝘇𝘂𝗻𝗱𝗮 ⚽)
𝗠𝗼𝘆𝗮𝗹𝗲 0️⃣➖1️⃣ 𝗦𝗶𝗹𝘃𝗲𝗿 ( 𝗜𝗻𝗻𝗼𝗰𝗲𝗻𝘁 S𝗵𝗲𝗺𝗮 ⚽)

```simmene ku Lee Lee```

KWAVUTA NDI KU MLAKHO WA ALOMWE😂😂😂mpakanatu mankhwala okuti Manchester United   - Sing'anga wina wachitapo gawo lake kut...
18/10/2026

KWAVUTA NDI KU MLAKHO WA ALOMWE😂😂😂

mpakanatu mankhwala okuti Manchester United - Sing'anga wina wachitapo gawo lake kuti mwinamwake masapota a man U adzimva kukoma😂😂

Tiphuzileko🤔🤔
18/10/2026

Tiphuzileko🤔🤔

18/10/2026

Kodi mwambi okuti "pawiri pawiri sipawuzilika" mu English ndi chan? 🤔🤔

Nthawi ikadalipo
18/10/2026

Nthawi ikadalipo

Address

Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Malawi wanga posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Organization

Send a message to Malawi wanga:

Shortcuts

Share