Bolani Chakwera
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Bolani Chakwera, Political organisation, Mzimba Street, Lilongwe.
31/05/2026
Lamulungu lopambana
Khalani M'modzi wa Ife Powuza Wina ndi Ena
30 June, 2026 Tikavote Mwa Unyinji
Inde Tumeni Ndavomera Ndikayimilire Inuyo
Ulendo Uno Tipose 8200 Votes Ija
Komaso Tinagwilizana Kale
Join my campaign today........
30/05/2026
Ayikatu mtsonkho pa Panadol, Bufen, Amoxicillin ndi mamkhwala ena amene timagwilitsa ntchito tsiku ndi tsiku. Economy ya Mwanamveka mukuiwona bwanji akuluakulu, atithandiza uyuyu koma?.
30/05/2026
10 pa 10 Dr Laz, 💪
Akamuna!!!!!
30/05/2026
LAGWA LOKHA BOMA LIJA KUNO!
Nde ena nkumati we are on the right track economically?
🤣🤣🤣🤣🤣
30/05/2026
Nde pali uchitsilu wina pa FB pano, Makhadethi sakumafuna kuti ulembe zoyipa za DPP ndi APM, ati tonse tizingowombela mmanja basi.FB yasandukanso ya Mulhakho? 🤣🤣🤣🤣
30/05/2026
PRESIDENT CHAKWERA TO ATTEND FUNERAL IN NKHATABAY
His Excellency Dr Lazarus Chakwera , the 6th President of the Republic of Malawi and President of the Malawi Congress Party (MCP), accompanied by the former First Lady, Madame Monica Chakwera , will today, Saturday, May 30th, 2026, attend the funeral of the late nephew of the former First Lady, Madame Monica Chakwera, in Nkhatabay District.
In accordance with our tradition, all those residing in Nkhatabay and surrounding areas are warmly invited and encouraged to join His Excellency in large numbers as he pays his final respects to the deceased. Your presence will provide comfort and support during this time around.
Click here to claim your Sponsored Listing.
Location
Category
Contact the business
Telephone
Website
Address
Mzimba Street
Lilongwe
AREA10
