Eeeeeh (kom mudzi uno
Ulipo ndithu et....?🤪🤪
Life is Long story
WELLCOM TO
LIFE IS LONG STORY
🇲🇼
mudzi wama
stories
❤️
LIFE IS LONG STORY
Mudzi wa ma stories
takulandirani simunachedwe popanga like
mwafika munthawi yake khalani omasuka
zikomo
😂😂😂😂
😜
🤪 🤪
🥴
mudzi onse uno
Landirani moni
panotu ndili
ku malawi
nde eeee
eheeee
Ndatolera chi story
mbambandetu...😁
kusowaku nde
ndi njara iyi
wachisoni
andigayire
kapero ka
chimanga...😹
moto ukumafuka
usiku okha okha
kuno Economy 😀🙄😜
kom nde
ndakusowani
AWELENGI...🥴🤔
ABWENZI ADZIKO LAPANSI
chapter 16
LYDEN, »dzidzidzi heiiii
kod umamwa madiragi..?
BWANJI ukuyankhura
Nonsense...? mesa iwe
Ndi amene wativulaza ife
Watibaya jekeseni....?😳🙊
Ndiwe chitsilu LYDEN
Ndipo ndipita ku police
Heiiii ndinakulakwilani
chani anthu inu...?
kundicheka chonchi
chifukwa chani....?
mwandicheka ndi
kumaliseche komwe
ndalakwa chani ine...?😭
ma doctor, »anayamba
kukokana kokana nawo
aPOLICE anatulukira ku
chipatala kuja ndi mabuku
“NTHAWI imeneyi mabuku
anali mu Unyoro....🥺
Edina, »chokha chongoti
Mabuku thaaa amvekere
Heiiii sir munthu wina ndi
Uyu amene amafunanso
kundigwililira winayo akuti
ndi Mark analipo anthu
atatu omwe amafuna
kundipanga chipongwe
ine...😭 💔 mwamwai
ndinakwanitsa kuthawa...💔😭
“aPOLICE, »anagwira
khosi la mabuku
amvekere ifetu timadziwa
kuti iweyo ndiye mwini
Film ndeno chimene
wapanga ndichani...?
kucheka tsikana moyipa
chonchi...?😏 ndiwe otani
nkhanza kupangila tsikana
Ngati Uyu...?
Mabuku, »anayamba
kulira milomo imangonjanja
kusowa choyankhula...😭 💔
SINE OLAKWA INE...😭 💔
NTHAWI YOMWEYO
Panatulukira mark pa
malowa ali pa wirotcheya
akumuyendetsa ndi Stella
Edina, »anangoti mark
thaaa amvekere ehee
INSPECTOR munthu wina
ndi Uyu, »Uyu nde tinafika
POLIMBANA ndi amene
anandicheka kumaliseche
mwamwayi ndinamulanda
mfuti ndikumuwombera
pa mtima...😭 💔
“Mark, »anayamba
kuzaza diso lili pa
nthunda amvekere...😂🤣
IKANI GAWO 16😁😹
mawa 8:00AM
ikuyambika..🥳🥳
HIE...?
kwangozi ziiiiiiiiii
kuchokera pa 12
June mpaka lero
No any stories
kwangoti ziiiii
Ena nkumaganiza
kuti ndidafa...😹😁
Ena nkumaganiza
kuti matama ena
nkumaganiza kuti
ndinatha...🫣😉
Ena nkumati adah
amenewa chilipo
chimene chinachitika
Lero nditalowa pa Fb
Ndapeza ma message
ochuluka kwambili...🙆😌
PEPANI KWANONSE
amene mumandikonda
kunena zoona munthune
Ndinayamba ndayima kulemba
ma stories pazifukwa munthune
ma busy amandichulukila maka
mwezi wathawu panopa nde
Bolani ndabweleranso mu
Graund😌😁😹🥳
ndeno kod
TIYAMBE film ina
Yanyuwani oro
tipitilize Film ya
ABWENZI ADZIKO LAPANSI
??????
😁
Oraaaaaa
Aubrey sankhan
🏝 is🔙
Eish 😓🙆
zikamachitika
ngati tikulotatu
achilima No more🥺
zokhudxatu izi...💔
13 is loading.........
😌i hope you are happy 😊
6:00pm
Click here to claim your Sponsored Listing.
Location
Category
Telephone
Website
Address
Lilongwe
