05/06/2026
Basi tukagona.
Be safe. And driver responsibly.
Directorate of Road Traffic and Safety Services (DRTSS) is a Department under the Ministry of Transport and Public Works (MoTPW).
It is charged with the responsibility of administering regulatory provisions governing the road transport industry in Malawi The Directorate of Road Traffic and Safety Services (DRTSS) is a Department under the Ministry of Transport and Public Works (MoTPW). It is charged with the responsibility of administering regulatory provisions governing the road transport industry in Malawi. The operations of the Directorate are guided by the Road Traffic Act (1997) and Road Traffic Regulations (2000).
05/06/2026
Basi tukagona.
Be safe. And driver responsibly.
05/06/2026
Ifeyo hoza Friday yathu Ili motele. Kuteteza inuyo from careless and reckless drivers. It's a calling
Nde mumwela pati
05/06/2026
Eee anthu muyenda ndi zinthu. Anyway, tatuluka.
This guy is ready for any attack 🙌
05/06/2026
MBWANDI!!!!!!!!!
Uyu wazepulidwa dzuwa likuswa mtengo ali ku waya.
Minibus imachedwa Passenger Service Vehicle, PSV, kutathawuza kuti ndiyonyamula Anthu.
Lorry imachedwa Goods Vehicle, GV, Kutathawuza kuti ikuyenela kunyamula katundu basi.
Mukanyamula Katundu ndi anthu mmalo amodzi mu minibus ngati mmene yapangila iyi, kosaloledwa.
Excuse me, let me ZEPU
05/06/2026
Lero tikuyendela akabaza, Ku Lunzu, Chileka, Chiradzulo ndi madela ena, kuwawunikila kuti njinga zawo apange regisita, komaso nawonso azayambeko kupangisa license.
Tinawuzaso kuti akamayenda pa nsewu azidekha, ndikuyenda mbali yawo osati kulowera paliponse.
Tili muliyenda kucheza ndi akabaza lero.
05/06/2026
🚸 ROAD SAFETY TIP FOR PREGNANT PASSENGERS
🤰 Buckle Up the Right Way – Protect Two Lives!
When pregnant, wearing a seatbelt correctly can significantly reduce the risk of injury to both mother and baby in the event of a crash.
✅ Place the lap belt low across the hips and below the baby bump, never over the stomach.
✅ Position the shoulder belt between the breasts and to the side of the bump.
❌ Never place the seatbelt across or above the abdomen, as it can cause serious injury during sudden braking or a collision.
Remember: Pregnancy is not a reason to avoid wearing a seatbelt. It is a reason to wear it correctly.
"A properly worn seatbelt protects both mother and unborn child."
Tikayime pati usiku uno?
How to navigate a 4 Ways
04/06/2026
Enforcement ili mkati.
Ena Akumatithawa. Ena kumatipasa moni. Koma wa Sienta sakumva Fadah. Anyway, tiyeni tiyende mosamala komaso mosunga malamulo
04/06/2026
Minibus yatapidwa chifukwa chonyamula Katundu wambiri komaso kunyamula anthu ndi katundu mu mmalo amodzi.
Galimoto ikalemera kwambiri imavuta kupanga control. Komaso ngati mwanyamula anthu ndi katundu Malo amodzi, katundu uja akasutha, or break ikapondedwa mwazizi, katundu uja umatha kugwela anthu.
Kaya tikumvana Kaya. Nde osapakila motele.
Excuse, let me ZEPU
| Monday | 07:30 - 16:30 |
| Tuesday | 07:30 - 16:30 |
| Wednesday | 07:30 - 16:30 |
| Thursday | 07:30 - 16:30 |
| Friday | 07:30 - 16:30 |
| Saturday | 08:00 - 12:00 |