01/07/2024
CHIVUMBULUTSO 2 : 21
Ndipo ndampatsa iye nthawi kuti alape; koma safuna kulapa kusiyana nacho chigololo chake.
For read more download the Bible using this link:
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Kubadwa mwasopano mwa mbuye, Library, Lilongwe.
01/07/2024
CHIVUMBULUTSO 2 : 21
Ndipo ndampatsa iye nthawi kuti alape; koma safuna kulapa kusiyana nacho chigololo chake.
For read more download the Bible using this link:
01/07/2024
MATEYU 12 : 12
Nanga kuposa kwake kwa munthu ndi nkhosa nkotani! Chifukwa cha ichi nkuloleka kuchita zabwino tsiku la Sabata.
For read more download the Bible using this link:
29/06/2024
YEREMIYA 29 : 11
Pakuti ndidziwa malingiriro amene ndilingiririra inu, ati Yehova, malingiriro a mtendere, si a choipa, akukupatsani inu adzukulu ndi chiyembekezero.
For read more download the Bible using this link: