Erifa Channel

Directions Website

Erifa Channel Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Erifa Channel, Public Service, Ntcheu.
(1)

23/10/2026

Mukutani?

22/10/2026

Nthawi ija mukawalangiza ija anawonetsa ngati kuti sanamve ayi ndithu anamva langizo lanu lija.. Lelo zikuwayendela chifukwa cha langizo lanu lija. Kusavomeleza pa maso panu kuja chifukwa choti amakupeputsani maso mwawo.
Akanawoneka opepela akanavomela pa maso pa inu.

Green 💚 dot recommended Yabwera chifukwa cha inu taziyamba tiyeni tisafoke
22/10/2026

Green 💚 dot recommended
Yabwera chifukwa cha inu taziyamba tiyeni tisafoke

Musayiwale kuwakodola anzanuwo apangire share, apangeni tag.Achinyamata anzanga let's wake up dziko ili likufuna ife .Do...
22/10/2026

Musayiwale kuwakodola anzanuwo apangire share, apangeni tag.

Achinyamata anzanga let's wake up dziko ili likufuna ife .
Don't save money invest your money
Ambiri tikulephera muzambiri chifukwa chosowekela Wisdom
Chifukwa Wisdom come from God
Koma tili ndi Knowledge from someone (school) akuti kuti uzachite bwino ukuyenela Kuma panga save ndalama kkkkk.
Munthu amene ali ndi Wisdom amaziwa kuti akamati save money ndi chani.
Ndikunena pano ena akuvutika koma ndalama yawo anapanga save ku bank.
Wina ndalama ngati yomweyo anapanga invest mu china chake.
Let's wait kwa anthuwa tizawone ma results ake

22/10/2026

Ndili ndi nkhani zambiri zoti ticheze koma mpata sindikumawupeza

22/10/2026

Mwina tingobwerezaso kapena muwauze ndinu ku comment section
Erifa Channel
Si page yomagawa ndalama pa Facebook kapena Kuma account a anthu ayiii.please. Wina akalandira Mphatso kapena ndalama pa mudzi pano chimakhala kuti chisomo cha Mulungu chamugwera
Erifa ali ngati mene muli inumo, nayeso ndimunthu amene akufuna thandizo kuchoka kwa anthu ena kuti mwina atakwanilitsa masomphenya ake.
Zinangovuta kuti Erifa anabadwa munthu wa chikondi.
Cholinga chathu chachikulu ndikufuna tizilimbikitsa kuti tikonze moyo wathu wa thupi komaso ku zimu.
Kuti tikamakhala pa dziko pano tisawoneke kuti ndife olephera ayii komaso kuti mwina pa tsiku la Ambuye tikakhale ndi choyankha.
By
Apostle Eric I love you all

22/10/2026

Mwadzuka bwanji abale anga pa mudzi pano.

21/10/2026

Akanakhala akudziwa kuti olakwa si ifee bwezi sakulankhula mene akulankhulilamu

21/10/2026

Fear not

Address

Ntcheu

Opening Hours

Monday 07:00 - 17:00
Tuesday 07:00 - 17:00
Wednesday 07:00 - 17:00
Thursday 07:00 - 17:00
Friday 07:00 - 17:00
Saturday 07:00 - 19:00

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Erifa Channel posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category