Bambo Poya akhala MP wathu kuyambira mu 2019, koma utsogoleri wake sunabweretse chitukuko chenicheni ku Zomba Ntonya. Mโmalo mopanga kuti anthu apindule ndi AIP (Affordable Input Programme), iye anangokhala busy kuthandiza atolankhani pomwe anthu ake ankavutika ndi njala komanso kusowa njira zothetsera kusowa chakudya.
Pamene njala inali pachimake, Masanga ndiye anaimira ndi anthu ake. Iye anagawa ma tonne oposa 60 a chimanga, kuti anthu apeze mpumulo. Komanso, Masanga wapereka mavaucha, omwe akupatsa anthu chiyembekezo kuti vuto la njala litha. Ndi mavauchawa, anthu adzatha kugula feteleza, kulima, komanso kupeza chimanga nthawi ya njala.
Chifukwa chokhacho chimene Masanga sali kugawa chimanga panopa ndi chakuti boma laletsa kugawa zakudya nthawi ya kampeni. Izi zikuwonetsa kulemekeza kwake malamulo, mosiyana ndi Poya yemwe ntchito yake ndi kuwononga ndondomeko za Masanga osati kuthandiza anthu.
Pa 16 September, tiyeni tipange chisankho cholondola. Tiyeni tichotse Bambo Poya amene watilephera, ndipo tisankhe Masanga, mtsogoleri amene ali ndi njira zenizeni zotithandiza kukhala odziyimira pawokha ku Zomba Ntonya.
YOUTH Alliance Zomba Ntonya
The Power of Young People to Change the World
23/08/2025
Hopping Masanga wabwera kudzatumikira abale ake. Ndipo Ena ayamba kupepetsa ๐๐๐
*๐ฒ๐ผZOMBA NTONYA*
*WOLEMBA TAMU ATOรDOLO*
*LATEST NEWS (AUGUST 20 2025)*
๐ฒ๐ผYemwe akuyima ngati phungu oyima payekha mdera la Zomba ntonya m'boma la Zomba, a Hoppings Chabwera Masanga wati adzayika chidwi chake kutukula umoyo ndi maphunziro, zomwe ati sizikuyenda bwino m'bomali, akadzasankhidwa pa 16 September.
Iwo anena izi Lachiwiri pomwe amakhazikitsa manifesto yawo kwa group seman kudelali,ma group osiyanasiyana anafika kunsonkhanowu monga a group chilipo komanso a group jalifu kuphatikiza apo anabwelanso mafumu opitilila 34,Iwo anapitiliza kunena Kuti adzakhala a kuthandiza anthu achikulile akadzapambana pa 16 September piano.
Pa nkhani ya umoyo, a masanga ati adzaonetsetsa ndi kulimbikitsa uchembere wabwino kwa amayi komanso chisamaliro cha ana.
Kunsonkhanowu kunalinso ma shadow Councillor wa ward ya Buleya ward Wisiki Bwaira maudzu komanso Councilor wa ulumba ward Patrick Saiti.
Pa nkhani yamaphunziro,a Hoppings Chabwera Masanga ati azidzapereka mphatso kwa aphunzitsi ngati njira yowalimbikitsa pa ntchito yawo komanso adzakulitsa njila zolimbikitsa ophunzira kuwerenga ndi kuwonetsetsa kuti mโsukulu muli zipangizo zophunzitsira ndi kuphunzilira zokwanira.
*Hoppings Chabwera Masanga*
*The game changer*
20/08/2025
Anthu akufutsa za komwe kunathera ndalama za msika wakwa Nachuma inu mukuwatumizira video ikuonetsa Ned Newmam Poya akugawa ma cheque
Tiyeni tilemekeze malamulo achitsankho
let's campaign without handout
*Countdown to polling day: 28 days to go*
๐ฒ๐ผ๐ฒ๐ผ๐ฒ๐ผ๐ฒ๐ผ๐ฒ๐ผ๐ฒ๐ผ๐ฒ๐ผ๐ฒ๐ผ๐ฒ๐ผ๐ฒ๐ผโ
โ
โ
โ
โ
โ
โ
โ
Ife chisankho ndiye tinapanga kale kuno ku Zomba Ntonya constituency kuti Hon Hoppings apite ku parliament pa 16 September pano ndipo akukwanila kukatiyimilila ife ANTHU a Zomba Ntonya, ndipo winanso ayi koma Hon Hoppings.
********************************************************************
โ
โ
โ
โ
โ
โ
โ
โ
โ
๐ฒ๐ผ๐ฒ๐ผ๐ฒ๐ผ๐ฒ๐ผ๐ฒ๐ผ๐ฒ๐ผ๐ฒ๐ผ๐ฒ๐ผ๐ฒ๐ผ
* HOPPINGS CHANWERA MASANGA*
* Ntonya | deserve better*
Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Hassan Chikhosi, Zavu Anord Chamanga, KidRude Mphamba, Rhozeck Paul, Seleman Alfred, Likkle Mark, Masters Angella, Kho Tchalos, Lexa Keleles, Redston Pataliya, Itz Izafat
03/08/2025
*๐ฒ๐ผHOPPINGS CHABWERA MASANGA*
*WOLEMBA TAMU ATOรDOLO*
*LATEST NEWS*
๐ฒ๐ผHoppings Chabwera Masanga, yemwe akufuna kudzaimira ngati phungu oyima payekha ku dera la zomba ntonya walonjeza kubweretsa zitukuko zosiyana-siyana.
Amasanga ati mwa zina adzathana ndi vuto la kusowa kwa chitetezo pogwira ntchito limodzi ndi achitetezo a m'mudzi komanso apolisi.
Iye walonjezanso kulumikizitsa anthu ochuluka ku madzi am'mipopi pofuna kukweza ukhondo, komanso kumanga chipatala ndi kubweretsa zipatala zoyenda-yenda, pofuna kupititsa patsogolo nkhani za umoyo.
Olemekezeka bwana Hoppings Chabwera Masanga apempha anthu kuti adzamuvotere iye, kuti athane ndi mavuto a zachuma omwe akuta kudelali
*Hoppings Chabwera Masanga*
*The game changer*
*ATOรDOLO*
15/07/2025
*Mvumbo wa Mphepo yakusintha pa ntchito zachitukuko ili paliponse mdera la Zomba Ntonya constituency Motsogozedwa ndi Phungu oyima payekha-Olemekezeka Bambo Hoppings Chabwera Masanga*
Olemekezeka Bambo Hoppings Chabwera Masanga ndi mmodzi mwa omwe akupikisana nawo pa mpando wa Phungu mdera la Zomba Ntonya. Monga mwadzina lawo, a Chabwera abwera mwa mphamvu, mwachikoka komanso mwachigonjetso pofuna kusintha mbiri ya Derali pakuti kwa nthawi yaitali, Bambo Hoppings Chabwera Masanga akhala akumva chisoni kuona delali likutsalila mu ntchito zachitukuko zambiri mpaka pano chifukwa a Phungu ake akhala akungolonjeza koma osakwanilitsa.
Olemekezeka Bambo Hoppings ndi Mtsogoleri yekhayo yemwe amadzipeleka chonse pofuna kuthandiza athu kotero kudzipeleka kwawo kwaima ngati chikwangwani chomwe chikulozera njira ya tsogolo lowala la Dera la Ntonya. Nthawi ya atsogoleri odzikonda omwe akhala akudya CDF ngati tomato yatha ndipo tayiponya kudzala, pano Maso athu ali pa kusintha zinthu mwanzeru ndi Olemekezeka Bambo Hoppings.
Pomaliza, nthawi yovotera chisoni, chizolowezi ingakhale kudziwika inatha, chaka chino tivotera chitukuko, kotero tiyeni tonseee mu chimvano cha mavu tikhale pambuyo ndikuvotera chitukuko chomwe chikubwera ndi Olemekezeka Bambo Hoppings Chabwera Masanga ngati MP wathu kudera lino la Ntonya constituency.
*Hon Hoppings Chabwera Masanga BOMA*
*Zomba Ntonya constituency | Imafunanso Zabwino*
๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐คบ๐คบ๐คบ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐คธโโ๏ธ๐คธโโ๏ธ๐คธโโ๏ธ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ช๐ช
08/04/2025
*LATEST NEWS*
๐ฒ๐ผProfessor Hoppings Chabwera Masanga ndi amene atazapambane pachisankho cha pa 16 September 2025 ku dela la zomba ntonya constituency.
Malinga ndi akaswiri pankhani zofufudza adera la Zomba ntonya atachita kafukufukuwawo apedza zoti phungu yemwe adzawine pa chisankho chomwe chidzachitike pa 16 September 2025 ndi Bwana Hoppings Chabwera Masanga
Potengera zomwe apedza mukafukufu ameneyu akuti ma shadow ena onse adzakhala pansi pa Hoppings Chabwera
Pali chiyembekedzo Choti ma percent ashadow ameneyi akhala akukwelabe mpaka tsiku lovota
*Hoppings Chabwera Masanga the game changer*
30/03/2025
Nkhani ndi malipoti ku Zomba Ntonya
๐ฒ๐ผChisankho Cha pa 16 September 2025 ndi mwayi waukulu kwa anthu a dera la zomba ntonya kuti asankhe mwanzeru posankha Shadow MP Hoppings chabwera masanga.
Ndipo lero Shadow MP woyima pa yekhayu akupitiridza ulendo wake woyendela ma Zone ku Zomba ntonya Constituency
Lero olemekezeka a Hoppings chabwera masanga anali akuyendela ma zone monga buleya zone,ntangatanga zone,Namatapa zone,chanda zone,thundu zone Komanso nathupi zone ndi ena ambiri mudelali.
Derali kuli ma Zone 32 ndi ma Center 27 Iyeyi akhala akuyendera derali pa matsiku 4 kuyambira zulo loweruka mpaka lachiwiri tsabata ya mawa.
Hoppings chabwera masanga ndi mayankho anu apa 16 September 2025 Ku zomba ntonya constituency.
Click here to claim your Sponsored Listing.
Location
Category
Contact the business
Telephone
Website
Address
Zomba
