The Tobacco Commission

Call Directions Website Contact the organization

The Tobacco Commission We regulate the to***co industry in Malawi, promoting the production and marketing of the country's green gold.

28/10/2026
17/10/2026

Kwa sabata zinayi, takhala tikukhomeretsa zitupa komanso kulemba alimi mu kalondolondo wa Know Your Grower (KYG) mmadera osiyanasiyana. Kukagwira ntchitoyi kufupi ndi kumene alimi amakhala ndi chimodzi cha zinthu zimene zakomera ambiri.

Awa ndi a Hendrix Billy Lihaka, a Mikongoni Estate, Engucwini EPA, ku Mzimba North kukambapo za ntchito imene takhala tikugwirayi:

16/10/2026

Kulembetsa mu kaundula wa KYG komanso kukhomera zitupa kupitirira ku ma ofesi a Commission. Mawa tingotseka registration komanso kukhomera kumene kukuchitika mmadera (field registration & licensing). Koma ku ma ofesi athu a ku Lilongwe, Limbe, Kasungu ndi Mzuzu ntchitoyi ipitirira.

Tsiku lotseka ntchitoyi ku ma ofesi athu tilengeza kutsogoloku.

Alimi onse ali ndi mwayi wolembetsa mu KYG komanso kukhomera zitupa.

Nali dongosolo la mmene tiyendere pamene taonjezera nthawi yokhomera zitupa komanso kulembetsa mu kaundula wa Know Your ...
02/10/2026

Nali dongosolo la mmene tiyendere pamene taonjezera nthawi yokhomera zitupa komanso kulembetsa mu kaundula wa Know Your Grower (KYG) mmadera osiyanasiyana.

Tikupempha alimi mugwiritse ntchito mwayi umenewu.

Taonjezera nthawi yokhomeretsera zitupa komanso kuchititsa KYG mmadera. Taonjezeranso madera amene tikafikire. Ndondomek...
01/10/2026

Taonjezera nthawi yokhomeretsera zitupa komanso kuchititsa KYG mmadera. Taonjezeranso madera amene tikafikire. Ndondomeko ya mmene tiyendere tikulengeza mma wayilesi osiyanasiyana komanso tipereka pa page ino.
Ministry of Agriculture - Malawi NASFAM TAMA Farmers Trust Agricultural Research and Extension Trust - ARET

KYG komanso kukhomera zitupa - Alimi amvetsa cholinga cha KYG.đź“· Lufita, Chitipa. Lero limeneli
24/09/2026

KYG komanso kukhomera zitupa - Alimi amvetsa cholinga cha KYG.

đź“· Lufita, Chitipa. Lero limeneli

Ndife wokondwa kuona kuti kalondolondo wa KYG komanso ntchito yokhomeretsa zitupa mmadera zikuyenda bwino. Alimi akufika...
23/09/2026

Ndife wokondwa kuona kuti kalondolondo wa KYG komanso ntchito yokhomeretsa zitupa mmadera zikuyenda bwino. Alimi akufika ku malo tikugwirira ntchito mwaunyinji. Aliyense akachita KYG ndiye kuti tateteza fodya wathu wa ku Malawi. Pogwira ntchito limodzi ndi mabungwe a alimi monga TAMA Farmers Trust NASFAM ndi ena, tikukwanitsa kufikira alimi ambiri ndi ma uthenga ofunika monga a KYG ndi zina.

It's exciting to see large turnouts at our field KYG and licensing centres. A full KYG will strengthen compliance and traceability in Malawi's to***co value chain. Through strong partnerships with grower associations, buying companies, Agricultural Research and Extension Trust - ARET and guidance from the Ministry of Agriculture - Malawi, we are making our industry more sustainable.

đź“· Chikwatula EPA, Ntchisi, Wednesday, 23/09/26

Ofunika kuchitiratu izi kuyambira mawali. Osadikira tsiku lotsiriza ayi.
20/09/2026

Ofunika kuchitiratu izi kuyambira mawali. Osadikira tsiku lotsiriza ayi.

Tikubwera kufupi ndi kwanu kudzakhomeretsa zitupa komanso kuchititsa kalondololondo wa alimi - Know Your Grower (KYG). A...
19/09/2026

Tikubwera kufupi ndi kwanu kudzakhomeretsa zitupa komanso kuchititsa kalondololondo wa alimi - Know Your Grower (KYG). Alimi onse TAMA Farmers Trust NASFAM ndi ena onse afike.

The el nino expected this year poses a challenge for to***co production in 2026/27 season. As such, no effort should be ...
11/09/2026

The el nino expected this year poses a challenge for to***co production in 2026/27 season. As such, no effort should be spared in cushioning our to***co production from the phenomenon.

We recently called industry leaders and players including Agricultural Research and Extension Trust - ARET TAMA Farmers Trust NASFAM, AHL and to***co buying companies to a meeting to discuss the el nino. The Ministry of Agriculture - Malawi was also represented. Read the story on https://tc.mw/to***co-industry-steps-up-el-nino-preparations/

Lilongwe University of Agriculture and Natural Resources Mwimba College of Agriculture

Address

Kanengo
Lilongwe
265

Opening Hours

Monday 07:30 - 16:30
Tuesday 07:30 - 16:30
Wednesday 07:30 - 16:30
Thursday 07:30 - 16:30
Friday 07:30 - 16:30

Telephone

+265998256545

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when The Tobacco Commission posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Organization

Send a message to The Tobacco Commission:

Shortcuts

Share